Psalms 10:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mumaima kutali nafe, Inu Chauta? Chifukwa chiyani mumabisala pamene tili pa mavuto?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muimiranji patali, Yehova? Mubisaliranji m'nyengo za nsautso?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chiyani Yehova mwayima patali? Chifukwa chiyani mukudzibisa nokha pa nthawi ya mavuto?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muimiranji patari, Yehova? Mubisaliranji m'nyengo za nsautso?