Psalms 10:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumtima mwake amaganiza kuti, “Mulungu sasamalako, waphimba maso ake, sadzaziwona zimenezi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anena m'mtima mwake, Mulungu waiwala; wabisa nkhope yake; sapenya nthawi zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amati mu mtima mwake, “Mulungu wayiwala, wabisa nkhope yake ndipo sakuonanso.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anena m'mtima mwace, Mulungu waiwala; Wabisa nkhope yace; sapenya nthawi zonse,