Psalms 10:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani munthu woipa amanyoza Mulungu? Chifukwa chiyani mumtima mwake amati, “Sadzandilanga?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Woipa anyozeranji Mulungu, anena m'mtima mwake, Simudzafunsira?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chiyani munthu woyipa amachitira chipongwe Mulungu? Chifukwa chiyani amati mu mtima mwake, “Iye sandiyimba mlandu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Woipa anyozeranii Mulungu, Anena m'mtima mwace, Simudzafunsira?