Psalms 10:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thetsani mphamvu za munthu woipa ndi wochimwa. Fufuzani kuipa kwake, ndipo mumlange kuti asadzabwerezenso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thyolani mkono wa woipa; ndipo wochimwa, mutsate choipa chake kufikira simuchipezanso china.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Thyolani dzanja la woyipitsitsa ndi la munthu woyipa; muzengeni mlandu chifukwa cha zoyipa zake zimene sizikanadziwika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Thyolani mkono wa woipa; Ndipo wocimwa, mutsate coipa cace kufikira simucipezanso cina.