Psalms 10:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndiye Mfumu mpaka muyaya. Mitundu ya anthu akunja idzatheratu m'dziko lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye Mfumu kunthawi yamuyaya; aonongeka amitundu m'dziko lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi Mfumu kwamuyaya; mitundu ya anthu idzawonongeka kuchoka mʼdziko lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye Mfumu ku nthawi yamuyaya; Aonongeka amitundu m'dziko lace.