Psalms 10:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potero mudzaŵateteza amasiye ndi opsinjidwa, kuti anthu amene ali a pansi pano, asadzathe kuwopsezanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti muweruze mlandu wa amasiye ndi wokhalira mphanthi, kuti munthu wa pa dziko lapansi angaonjeze kuopsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuteteza ana amasiye ndi oponderezedwa, ndi cholinga chakuti munthu amene ali wa dziko lapansi asaopsenso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti muweruze mlandu wa amasiye ndi wokhalira mphanthi, Kuti munthu wa pa dziko lapansi angaonjeze kuopsa.