Psalms 10:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja munthu woipa amanyadira zokhumba za mtima wake, wokonda chuma amanyoza ndi kukana Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti woipa adzitamira chifuniro cha moyo wake, adalitsa wosirira, koma anyoza Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amatamandira zokhumba za mu mtima wake; amadalitsa aumbombo ndi kuchitira chipongwe Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti woipa adzitamira cifuniro ca moyo wace, Adalitsa wosirira, koma anyoza Yehova.