Psalms 10:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu woipa sasamala Mulungu chifukwa cha kunyada kwake. Mumtima mwake amati, “Kulibe Mulungu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Woipa, monga mwa kudzikuza kwa nkhope yake, akuti, Sadzafunsira. Malingaliro ake onse akuti, Palibe Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa kunyada kwake woyipa safunafuna Mulungu; mʼmaganizo ake wonse mulibe malo a Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Woipa, monga mwa kudzikuza kwa nkhope yace, akuti, Sadzafunsira. Malingaliro ace onse akuti, Palibe Mulungu.