Psalms 10:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalalira m'midzi, amapha anthu osalakwa m'malo obisalira. Amazondazonda kuti apeze opanda mwai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akhala m'molalira midzi; mobisalamo akupha munthu wosachimwa. Ambisira waumphawi nkhope yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amabisalira anthu pafupi ndi midzi, kuchokera pobisalapo amapha anthu osalakwa, amayangʼanayangʼana mwachinsinsi anthu oti awawononge.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akhala m'molalira midzi; Mobisalamo akupha munthu wosacimwa: Ambisira waumphawi nkhope yace,