Psalms 100:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Fuulani kwa Chauta ndi chimwemwe, inu maiko onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Chiyamiko. Fuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo. Nyimbo yothokoza. Fuwulani kwa Yehova mwachimwemwe, inu dziko lonse lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pfuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi.