Psalms 100:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Iye ndi wabwino. Chikondi chake nchamuyaya, kukhulupirika kwake nkosatha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova ndiye wabwino; chifundo chake chimanka muyaya; ndi chikhulupiriko chake ku mibadwomibadwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova ndi wabwino ndipo chikondi chake ndi chamuyaya; kukhulupirika kwake nʼkokhazikika pa mibado ndi mibado.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova ndiye wabwino; cifundo cace cimamka muyaya; Ndi cikhulupiriko cace ku mibadwo mibadwo.