Psalms 101:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu okhulupirika am'dziko, ndidzaŵayang'ana moŵakomera mtima, ndipo adzakhala ndi ine. Oyenda m'njira yopanda cholakwa adzanditumikira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maso anga ayang'ana okhulupirika m'dziko, kuti akhale ndi Ine; iye amene ayenda m'njira yangwiro, iyeyu adzanditumikira Ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso anga adzakhala pa okhulupirika mʼdziko, kuti akhale pamodzi ndi ine; iye amene mayendedwe ake ndi wosalakwa adzanditumikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maso anga ayang'ana okhulupirika m'dziko, kuti akhale ndi Ine; Iye amene ayenda m'njira yangwiro, iyeyu adzanditumikira Ine.