Psalms 101:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe munthu wochita zonyenga amene adzakhale m'nyumba mwanga. Palibe munthu wolankhula zabodza amene adzakhale pafupi ndi ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wakuchita chinyengo sadzakhala m'kati mwa nyumba yanga; wakunena mabodza sadzakhazikika pamaso panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aliyense wochita chinyengo sadzakhala mʼnyumba mwanga. Aliyense woyankhula mwachinyengo sadzayima pamaso panga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wakucita cinyengo sadzakhala m'kati mwa nyumba yanga; Wakunena mabodza sadzakhazikika pamaso panga.