Psalms 101:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsiku ndi tsiku ndidzaononga oipa onse am'dziko. Onse ochita zoipa ndidzaŵachotsa mu mzinda wa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mamawa onse ndidzadula oipa onse a m'dziko; kuduliratu onse akuchita zopanda pake kumudzi wa Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa uliwonse ndidzatontholetsa anthu onse oyipa mʼdziko; ndidzachotsa aliyense wochita zoyipa mu mzinda wa Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mamawa onse ndidzadula oipa onse a m'dziko; Kuduliratu onse akucita zopanda pace ku mudzi wa Yehova.