Psalms 102:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa cha ukali wanu ndi mkwiyo wanu, popeza kuti Inu mwandinyamula ndi kunditaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa cha ukali wanu ndi kuzaza kwanu; popeza munandinyamula ndipo munandigwetsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa cha ukali wanu waukulu, popeza Inu mwandinyamula ndi kunditayira kumbali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca ukali wanu ndi kuzaza kwanu; Popeza munandinyamula ndipo munandigwetsa.