Psalms 102:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu Chauta, mumakhala pa mpando wanu waufumu mpaka muyaya. Anthu a mibadwo yonse adzakukumbukirani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu, Yehova, mukhalabe kunthawi yonse; ndi chikumbukiro chanu ku mibadwomibadwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Yehova, muli pa mpando wanu waufumu kwamuyaya; kudziwika kwanu ndi kokhazikika ku mibado yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu, Yehova, mukhalabe ku nthawi yonse; Ndi cikumbukilo canu ku mibadwo mibadwo.