Psalms 102:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzadzuka nkuchitira chifundo mzinda wa Ziyoni, zoonadi, nthaŵi yake youkomera mtima yafika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu mudzauka, ndi kuchitira nsoni Ziyoni; popeza yafika nyengo yakumchitira chifundo, nyengo yoikika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mudzadzuka ndi kuchitira chifundo Ziyoni pakuti ndi nthawi yoti muonetse kukoma mtima kwanu pa iyeyo; nthawi yoyikika yafika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu mudzauka, ndi kucitira nsoni Ziyoni; Popeza yafika nyengo yakumcitira cifundo, nyengo yoikika.