Psalms 102:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mzindawo amaukondabetu anthu anu, ngakhale waonongeka ndi kusanduka bwinja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti atumiki anu akondwera nayo miyala yake, nachitira chifundo fumbi lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti miyala yake ndi yokondedwa kwa atumiki anu; fumbi lake lokha limawachititsa kuti amve chisoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti atumiki anu akondwera nayo miyala yace, Nacitira cifundo pfumbi lace.