Psalms 102:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitundu ya anthu idzalemekeza Chauta moopa, mafumu onse a pa dziko lapansi adzaopa ulemerero wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo amitundu adzaopa dzina la Yehova, ndi mafumu onse a dziko lapansi ulemerero wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitundu ya anthu idzaopa dzina la Yehova, mafumu onse a dziko lapansi adzalemekeza ulemerero wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo amitundu adzaopa dzina la Yehova, Ndi mafumu onse a dziko lapansi ulemerero wanu;