Psalms 102:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzamanganso Ziyoni, ndipo adzaonekera mu ulemerero wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova anamanga Ziyoni, anaoneka m'ulemerero wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova adzamanganso Ziyoni ndi kuonekera mu ulemerero wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova anamanga Ziyoni, Anaoneka m'ulemerero wace;