Psalms 102:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zilembedwe chifukwa cha mbadwo wakutsogolo, kuti anthu amene mpaka tsopano lino sanabadwebe, nawonso adzatamande Chauta,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi adzachilembera mbadwo ukudza; ndi mtundu wa anthu umene udalengedwa udzamlemekeza Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimenezi zilembedwe chifukwa cha mibado ya mʼtsogolo, kuti anthu amene sanabadwe adzatamande Yehova:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici adzacilembera mbadwo ukudza; Ndi mtundu wa anthu umene udalengedwa udzamlemekeza Yehova.