Psalms 102:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adayang'ana pansi ali m'malo ake oyera kumwamba, ali kumwambako, Chauta adayang'ana pa dziko lapansi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anapenya pansi ali kumwamba kuli malo ake opatulika; Yehova pokhala kumwamba anapenya dziko lapansi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova anayangʼana pansi kuchokera ku malo ake opatulika mmwamba, kuchokera kumwamba anayangʼana dziko lapansi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anapenya pansi ali kumwamba kuli malo ace opatulika; Yehova pokhala kumwamba anapenya dziko lapansi;