Psalms 102:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu adzalalika dzina la Chauta ku Ziyoni, ndipo adzamtamanda ku Yerusalemu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti anthu alalikire dzina la Yehova m'Ziyoni, ndi chilemekezo chake m'Yerusalemu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero dzina la Yehova lidzalengezedwa mu Ziyoni ndi matamando ake mu Yerusalemu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti anthu alalikire dzina la Yehova m'Ziyoni, Ndi cilemekezo cace m'Yerusalemu;