Psalms 102:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pamene mitundu ya anthu ndi mafumu adzasonkhana kuti apembedze Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Posonkhana pamodzi mitundu ya anthu, ndi maufumu kuti atumikire Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamene mitundu ya anthu ndi maufumu adzasonkhana kuti alambire Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Posonkhana pamodzi mitundu ya anthu, Ndi maufumu kuti atumikire Yehova.