Psalms 102:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudaika maziko a dziko lapansi kalekale, ndipo zakumwamba mudazipanga ndi manja anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munakhazika dziko lapansi kalelo; ndipo zakumwamba ndizo ntchito ya manja anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pachiyambi Inu munakhazikitsa maziko a dziko lapansi ndipo mayiko akumwamba ndi ntchito ya manja anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munakhazika dziko lapansi kalelo; Ndipo zakumwamba ndizo nchito ya manja anu.