Psalms 102:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masiku anga amangopita ngati utsi, ndipo thupi langa likuyaka ngati ng'anjo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza masiku anga akanganuka ngati utsi, ndi mafupa anga anyeka ngati nkhuni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti masiku anga akupita ngati utsi; mafupa anga akunyeka ngati nkhuni zoyaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza masiku anga akanganuka ngati utsi, Ndi mafupa anga anyeka ngati nkhuni.