Psalms 102:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga wakanthidwa, ndipo wafota ngati udzu, zoonadi, ngakhale chakudya chimandinyansa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wanga ukunga udzu womweta, nufota; popeza ndiiwala kudya mkate wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga wakanthidwa ndipo ukufota ngati udzu; ndipo ndimayiwala kudya chakudya changa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wanga ukunga udzu wamweta, nufota; Popeza ndiiwala kudya mkate wanga.