Psalms 102:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndaonderatu ngati munthu wachitopa, ntchito yanga ndi kubuula nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha liu la kubuula kwanga mnofu wanga umamatika kumafupa anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha kubuwula kwanga kofuwula ndatsala chikopa ndi mafupa okhaokha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca liu la kubuula kwanga Mnofu wanga umamatika ku mafupa anga.