Psalms 102:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndili ngati mbalame yakuchipululu, ngati kadzidzi wam'mabwinja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikunga vuwo m'chipululu; ndikhala ngati kadzidzi wa kumabwinja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndili ngati kadzidzi wa ku chipululu, monga kadzidzi pakati pa mabwinja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikunga bvuwo m'cipululu; Ndikhala ngati kadzidzi wa kumabwinja.