Psalms 102:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inetu ndimadya phulusa ngati chakudya, chakumwa changa ndimasakaniza ndi misozi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndadya mapulusa ngati mkate, ndi kusanganiza chomwera changa ndi misozi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndimadya phulusa ngati chakudya changa ndi kusakaniza chakumwa changa ndi misozi
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndadya mapulusa ngati mkate, Ndi kusanganiza-comwera canga ndi misozi,