Psalms 103:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Satilanga moyenerera machimo athu, satibwezera molingana ndi zolakwa zathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sanatichitira monga mwa zolakwa zathu, kapena kutibwezera monga mwa mphulupulu zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
satichitira molingana ndi machimo athu, kapena kutibwezera molingana ndi mphulupulu zathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sanaticitira monga mwa zolakwa zathu, Kapena kutibwezera monga mwa mphulupulu zathu.