Psalms 103:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, ndi momwenso chidakulira chikondi chake chosasinthika kwa anthu oopa Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti monga m'mwamba mutalikira ndi dziko lapansi, motero chifundo chake chikulira iwo akumuopa Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, koteronso chikondi chake nʼchachikulu kwa iwo amene amamuopa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti monga m'mwamba mutalikira ndi dziko lapansi, Motero cifundo cace cikulira iwo akumuopa Iye.