Psalms 103:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga kuvuma kuli kutali ndi kuzambwe, ndi momwenso amachotsera zolakwa zathu kuti zikhale kutali ndi ife.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga kum'mawa kutanimpha ndi kumadzulo, momwemo anatisiyanitsira kutali zolakwa zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
monga kummawa kutalikirana ndi kumadzulo, koteronso Iye watichotsera mphulupulu zathu kuti zikhale kutali nafe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga kum'mawa kutanimpha ndi kumadzulo, Momwemo anatisiyanitsira kutali zolakwa zathu.