Psalms 103:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kunena za munthu, masiku ake sakhalitsa, ali ngati a udzu, munthuyo amakondwa ngati duŵa lakuthengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munthu, masiku ake akunga udzu; aphuka monga duwa la kuthengo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kunena za munthu, masiku ake ali ngati udzu, amaphuka ngati duwa la mʼmunda;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munthu, masiku ace akunga udzu; Aphuka monga duwa la kuthengo.