Psalms 103:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthuwo ndi amene amasunga chipangano chake, amene amakumbukira kusunga malamulo ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kwa iwo akusunga chipangano chake, ndi kwa iwo akukumbukira malangizo ake kuwachita.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
iwo amene amasunga pangano lake ndi kukumbukira kumvera malangizo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwa iwo akusunga cipangano cace, Ndi kwa iwo akukumbukila malangizo ace kuwacita.