Psalms 103:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta wakhazikitsa mpando wake wachifumu kumwamba, ndipo amalamulira zonse mu ufumu wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova anakhazika mpando wachifumu wake Kumwamba; ndi ufumu wake uchita mphamvu ponsepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova wakhazikitsa mpando wake waufumu mmwamba ndipo ufumu wake umalamulira onse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova anakhazika mpando wacifumu wace Kumwamba; Ndi ufumu wace ucita mphamvu ponsepo,