Psalms 103:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye amene amakupatsa zabwino nthaŵi zonse za moyo wako, choncho umakhalabe wa mphamvu zatsopano ngati mphungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene akhutitsa m'kamwa mwako ndi zabwino; nabweza ubwana wako unge mphungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene akwaniritsa zokhumba zako ndi zinthu zabwino, kotero kuti umakhala wamphamvu zatsopano ngati mphungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene akhutitsa m'kamwa mwako ndi zabwino; Nabweza ubwana wako unge mphungu.