Psalms 103:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta ndi wachifundo ndi wokoma mtima, ndi wosakwiya msanga, ndipo chikondi chake chosasinthika nchachikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova ndiye wa nsoni zokoma ndi wachisomo, wosakwiya msanga, ndi wa chifundo chochuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova ndi wachifundo ndi wokoma mtima, wosakwiya msanga ndi wachikondi chochuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova ndiye wa nsoni zokoma ndi wacisomo, Wosakwiya msanga, ndi wa cifundo cocuruka.