Psalms 103:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akatikalipira, mkwiyo wake sudzakhala woyaka mpakampaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sadzatsutsana nao nthawi zonse; ndipo sadzasunga mkwiyo wake kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye sadzatsutsa nthawi zonse, kapena kusunga mkwiyo wake kwamuyaya;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sadzatsutsana nao nthawi zanse; Ndipo sadzasunga mkwiyo wace kosatha.