Psalms 104:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamanda Chauta, iwe mtima wanga. Inu Chauta, Mulungu wanga, ndinu aakulu kwambiri. Mumavala ulemu ndi ufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lemekeza Yehova, moyo wanga; Yehova, Mulungu wanga, Inu ndinu wamkulukulu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tamanda Yehova, iwe moyo wanga. Inu Yehova Mulungu wanga, ndinu wamkulu kwambiri; mwavala ulemerero ndi ufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lemekeza Yehova, moyo wanga; Yehova, Mulungu wanga, Inu ndinu wamkurukuru;