Psalms 104:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbalame zimamanga zisa pafupi ndi mitsinjeyo, zimaimba m'nthambi za mitengo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbalame za mlengalenga zifatsa pamenepo, zimaimba pakati pa mitawi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbalame zamlengalenga zimayika zisa mʼmbali mwa madzi; zimayimba pakati pa thambo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbalame za mlengalenga zifatsa pamenepo, Zimayimba pakati pa mitawi.