Psalms 104:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumathirira mapiri ndi madzi ochokera ku malo anu akumwamba. Dziko lapansi ladzaza ndi madalitso anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye amwetsa mapiri mochokera m'zipinda zake: Dziko lakhuta zipatso za ntchito zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amathirira mapiri kuchokera ku zipinda zake zapamwamba; dziko lapansi limakhutitsidwa ndi chipatso cha ntchito yake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye amwetsa mapiri mocokera m'zipinda zace: Dziko lakhuta zipatso za nchito zanu.