Psalms 104:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitengo ya Chauta amaithirira ndi madzi ambiri, mikungudza ya ku Lebanoni imene adaibzala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mitengo ya Yehova yadzala ndi madzi; mikungudza ya ku Lebanoni imene anaioka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitengo ya Yehova ndi yothiriridwa bwino, mikungudza ya ku Lebanoni imene Iye anadzala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mitengo ya Mulungu yadzala ndi madzi; Mikungudza ya ku Lebano imene anaioka;