Psalms 104:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbalame zimamanga zisa m'menemo, dokowe amamanga chisa m'mikungudzamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
m'mwemo mbalame zimanga zisa zao; pokhala chumba mpa mitengo ya mikungudza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbalame zimamanga zisa zawo; kakowa ali ndi malo ake mʼmikungudzamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo mbalame zimanga zisa zao; Pokhala cumba mpa mitengo ya mikungudza,