Psalms 104:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumadzifunditsa ndi kuŵala ngati chovala, mwatambasula mlengalenga ngati hema.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
muvala ulemu ndi chifumu. Amene mudzikuta nako kuunika monga ndi chovala; ndi kuyala thambo ngati nsalu yotchinga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye wadzifunditsa kuwala ngati chovala; watambasula miyamba ngati tenti
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mubvala ulemu ndi cifumu. Amene mudzikuta nako kuunika monga ndi cobvala; Ndi kuyala thambo ngati nsaru yocinga;