Psalms 104:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Misona ya mikango imabangula pofunafuna nyama, kupempha chakudya kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Misona ya mkango ibangula potsata nyama yao, nifuna chakudya chao kwa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikango imabangula kufuna nyama, ndi kufunafuna chakudya chawo kuchokera kwa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Misona ya mkango ibangula potsata nyama yao, Nifuna cakudya cao kwa Mulungu.