Psalms 104:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dzuŵa likamatuluka, imabwerera nkukagona m'mapanga mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potuluka dzuwa, zithawa, zigona pansi m'ngaka mwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuwa limatuluka ndipo iyo imapita kukabisala; imabwerera kukagona pansi mʼmapanga awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Poturuka dzuwa, zithawa, Zigona pansi m'ngaka mwao.