Psalms 104:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta ntchito zanu nzambiri, zonse mwazipanga mwanzeru, ndipo dziko lapansi ladzaza ndi zolengedwa zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ntchito zanu zichulukadi, Yehova! Munazichita zonse mwanzeru; dziko lapansi lidzala nacho chuma chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ntchito zanu ndi zochulukadi Inu Yehova! Munazipanga zonse mwanzeru, dziko lapansi ladzaza ndi zolengedwa zanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nchito zanu zicurukadi, Yehova! Munazicita zonse mwanzeru; Dziko lapansi lidzala naco cuma canu.