Psalms 104:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwamanga Nyumba yanu pa madzi akumwamba, mitambo yaliŵiro ili ngati galeta lanu, mumayenda pa mapiko a mphepo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene alumikiza mitanda ya zipinda zake m'madzi; naika makongwa akhale agaleta ake; nayenda pa mapiko a mphepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo wayika pa madzi mitanda ya chipinda chake. Iye amasandutsa mitambo kukhala galeta lake, ndi kuwuluka pa mapiko a mphepo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene alumikiza mitanda ya zipinda zace m'madzi; Naika makongwa akhale agareta ace; Nayenda pa mapiko a mphepo;