Psalms 104:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaimbira Chauta moyo wanga wonse. Ndidzaimba nyimbo zotamanda Chauta, nthaŵi zonse pamene ndili moyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzaimbira Yehova m'moyo mwanga: ndidzaimbira Mulungu wanga zomlemekeza pokhala ndilipo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzayimbira Yehova moyo wanga wonse; ndidzayimbira matamando Mulungu wanga nthawi yonse imene ndili ndi moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzayimbira Yehova m'moyo mwanga: Ndidzayimbira Mulungu wanga zomlemekeza pokhala ndiripo.